Amuna awiri akuphunzira Baibulo

Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Baibulo limafotokoza chinsinsi cha mmene mungakhalire ndi moyo wosangalatsadi.


Ino ndi webusaiti yovomerezeka ya zikhulupiriro, ziphunzitso ndi ntchito za Mboni za Yehova. Bungwe la Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc. ndi bungwe lovomerezeka limene Mboni za Yehova zimagwiritsa ntchito.

Malemba amene tawagwiritsira ntchito akuchokera m’Baibulo la Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, Kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

Pempho Lathu kwa Inu

Kodi mukufuna kumaphunzira Baibulo panyumba panu kuti muwonjezere zimene mumadziwa kale za m’Baibulo?

Werengani Baibulo pa Intaneti

Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Kaya ndife anthu otani, Baibulo lili ndi malangizo ndi uphungu wofunika. Muziliwerenga tsiku ndi tsiku.

Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo

Yesu akucheza ndi kamnyamata

Ili ndi bukhu la nkhani zenizeni. Zatengedwa m’bukhu lalikulu koposa, Baibulo.


Kodi Mukufuna Kudziwa Choonadi?

Mayi akuphunzira zimene Baibulo limaphunzitsa

Choonadi chokhudza chiyani? Cha mafunso ofunika kwambiri amene anthu amafuna kudziwa mayankho ake.


Mapeto a Chipembedzo Chonyenga Ayandikira!

Mkazi wachiwerewere

Kodi chipembedzo chonyenga n’chiyani? Kodi inuyo zidzakukhudzani motani?